Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Timoteyo 2:6 - Buku Lopatulika

6 Wam'munda wogwiritsitsa ntchitoyo ayenera akhale woyamba kulandira zipatsozo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Wam'munda wogwiritsitsa ntchitoyo ayenera akhale woyamba kulandira zipatsozo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Mlimi wogwira ntchitoyo molimbika, ndiye ayenera kukhala woyamba kulandira nao zipatso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Mlimi wolimbika ndi amene amayembekezereka kukhala woyambirira kulandira gawo la zokolola.

Onani mutuwo Koperani




2 Timoteyo 2:6
14 Mawu Ofanana  

Wosunga mkuyu adzadya zipatso zake; wosamalira ambuyake adzalemekezedwa.


Pakuti Ufumu wa Kumwamba ufanana ndi munthu mwini banja, amene anatuluka mamawa kukalembera antchito a m'munda wake wampesa.


Pomwepo uyo amene analandira matalente asanu, anapita kugula nazo malonda, napindulapo matalente ena asanu.


Ndipo ananena kwa iwo, Dzinthu dzichuluka, koma antchito achepa; potero pemphani Mwini dzinthu, kuti akankhe antchito kukututa kwake.


Koma ndichita zonse chifukwa cha Uthenga Wabwino, kuti ndikakhale woyanjana nao.


Lingirira chimene ndinena; pakuti Ambuye adzakupatsa chidziwitso m'zonse.


Pakuti chikusowani chipiriro, kuti pamene mwachita chifuniro cha Mulungu, mukalandire lonjezano.


Pakuti nthaka imene idamwa mvula iigwera kawirikawiri, nipatsa therere loyenera iwo amene adailimira, ilandira dalitso lochokera kwa Mulungu:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa