2 Samueli 9:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo iye anamlambira, nati, Mnyamata wanu ndani, kuti mulikupenya galu wakufa monga ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo iye anamlambira, nati, Mnyamata wanu ndani, kuti mulikupenya galu wakufa monga ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Iyeyo adamuŵeramira, nati, “Kodi ine mtumiki wanu ndine yani, kuti musamale galu wakufa ngati ine?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mefiboseti anawerama pansi ndipo anati, “Mtumiki wanu ndine yani kuti musamale galu wakufa ngati ine?” Onani mutuwo |