2 Samueli 9:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mefiboseti anawerama pansi ndipo anati, “Mtumiki wanu ndine yani kuti musamale galu wakufa ngati ine?” Onani mutuwoBuku Lopatulika8 Ndipo iye anamlambira, nati, Mnyamata wanu ndani, kuti mulikupenya galu wakufa monga ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo iye anamlambira, nati, Mnyamata wanu ndani, kuti mulikupenya galu wakufa monga ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Iyeyo adamuŵeramira, nati, “Kodi ine mtumiki wanu ndine yani, kuti musamale galu wakufa ngati ine?” Onani mutuwo |
Abineri anakwiya kwambiri chifukwa cha zimene Isi-Boseti ananena ndipo anamuyankha kuti “Kodi ukuyesa ndine mutu wagalu umene ali mbali ya Ayuda? Lero lino ndine wokhulupirika ku nyumba ya abambo ako, Sauli ndi banja lake ndi anzake. Ine sindinakupereke kwa Davide, koma tsopano ukundinena pa cholakwa chimene ndachita pa mkazi uyu!