2 Samueli 9:5 - Buku Lopatulika5 Pamenepo mfumu Davide anatumiza anthu nakatenga iye kunyumba ya Makiri mwana wa Amiyele ku Lodebara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamenepo mfumu Davide anatumiza anthu nakatenga iye kunyumba ya Makiri mwana wa Amiyele ku Lodebara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pamenepo mfumu Davide adatuma anthu kuti akamtenge, ndipo iwo adakamtengadi ku nyumba ya Makiri mwana wa Amiyele, ku Lodebara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Kotero mfumu inamubweretsa kuchokera ku Lodebara, ku nyumba ya Makiri mwana wa Amieli. Onani mutuwo |