Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 9:5 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Kotero mfumu inamubweretsa kuchokera ku Lodebara, ku nyumba ya Makiri mwana wa Amieli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

5 Pamenepo mfumu Davide anatumiza anthu nakatenga iye kunyumba ya Makiri mwana wa Amiyele ku Lodebara.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Pamenepo mfumu Davide anatumiza anthu nakatenga iye kunyumba ya Makiri mwana wa Amiyele ku Lodebara.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Pamenepo mfumu Davide adatuma anthu kuti akamtenge, ndipo iwo adakamtengadi ku nyumba ya Makiri mwana wa Amiyele, ku Lodebara.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 9:5
3 Mawu Ofanana  

ndipo anaona mʼbado wachitatu wa ana a Efereimu. Yosefe anatenganso ana a Makiri, mwana wa Manase kukhala ngati ana a mʼbanja lake.


Mfumu inafunsa kuti, “Ali kuti?” Ziba anayankha kuti, “Iye ali ku nyumba ya Makiri mwana wa Amieli ku Lodebara.”


Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Sauli atafika kwa Davide, anawerama pansi kupereka ulemu kwa iye. Davide anati, “Mefiboseti!” Iye anayankha kuti, “Ine mtumiki wanu.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa