2 Samueli 8:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Davide anamveketsa dzina lake pamene anabwera uko adakantha Aaramu mu Chigwa cha Mchere, ndiwo anthu zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Davide anamveketsa dzina lake pamene anabwera uko adakantha Aaramu m'Chigwa cha Mchere, ndiwo anthu zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mbiri ya Davide idamveka ponseponse. Pamene ankabwerera, anali atapha Aedomu 18,000 ku chigwa cha Mchere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndipo Davide anatchuka atabwera kokakantha Aedomu 18,000 mu Chigwa cha Mchere. Onani mutuwo |