2 Samueli 8:12 - Buku Lopatulika12 za Aaramu, za Amowabu, za ana a Amoni, za Afilisti, za Amaleke, ndi zofunkha za Hadadezere, mwana wa Rehobu mfumu ya ku Zoba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 za Aaramu, za Amowabu, za ana a Amoni, za Afilisti, za Amaleke, ndi zofunkha za Hadadezere, mwana wa Rehobu mfumu ya ku Zoba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Anthuwo anali Aedomu, Amowabu, Aamoni, Afilisti ndi Aamaleke. Zina zinali zimene adaafunkha kwa Hadadezere mwana wa Rehobu, mfumu ya ku Zoba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Edomu ndi Mowabu, Aamoni ndi Afilisti, ndi Aamaleki. Iye anaperekanso zolanda ku nkhondo zochokera kwa Hadadezeri mwana wa Rehobu, mfumu ya Zoba. Onani mutuwo |