2 Samueli 8:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo m'tsogolo mwake Davide anakantha Afilisti, nawagonjetsa Davide nalanda mudzi wa Metege Ama m'manja mwa Afilisti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo m'tsogolo mwake Davide anakantha Afilisti, nawagonjetsa Davide nalanda mudzi wa Metege Ama m'manja mwa Afilisti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake Davide adathira nkhondo Afilisti, naŵagonjetsa, ndipo adaŵalanda mzinda wa Metegama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Patapita nthawi, Davide anagonjetsa Afilisti ndi kuwapambana ndipo analanda Metegi Ama kuchoka mʼmanja mwa Afilistiwo. Onani mutuwo |