2 Samueli 7:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo tsopano, Yehova Mulungu, Inu ndinu Mulungu, ndi mau anu adzakhala oona, ndipo Inu munalonjezana ndi mnyamata wanu kumchitira chabwino ichi, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo tsopano, Yehova Mulungu, Inu ndinu Mulungu, ndi mau anu adzakhala oona, ndipo Inu munalonjezana ndi mnyamata wanu kumchitira chabwino ichi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Ndipo tsopano Inu Chauta Wamphamvuzonse, ndinu Mulungu, ndipo mau anu ngoona. Mwalonjeza kuti mudzandichitira zabwino zotere ine mtumiki wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Inu Ambuye Wamphamvuzonse, ndinu Mulungu! Mawu anu ndi odalirika, ndipo mwalonjeza zinthu zabwinozi kwa mtumiki wanu. Onani mutuwo |