2 Samueli 7:17 - Buku Lopatulika17 Monga mwa mau onse awa ndi monga mwa masomphenya onse awa, momwemo Natani analankhula ndi Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Monga mwa mau onse awa ndi monga mwa masomphenya onse awa, momwemo Natani analankhula ndi Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Natani adalankhula ndi Davide potsata mau onseŵa, ndiponso potsata zimene adaziwona m'masomphenyaŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Natani anafotokozera Davide mawu onse avumbulutso limene analandira. Onani mutuwo |