2 Samueli 6:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo pofika iwo ku dwale la Nakoni, Uza anatambasula dzanja lake, nachirikiza likasa la Mulungu; chifukwa ng'ombe zikadapulumuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo pofika iwo ku dwale la Nakoni, Uza anatambasula dzanja lake, nachirikiza likasa la Mulungu; chifukwa ng'ombe zikadapulumuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ndipo atafika pa malo opunthirapo tirigu ku Nakoni, ng'ombe zidaafuna kugwa, ndiye Uza nkutambalitsa dzanja kuti agwirire Bokosi la Mulungu lija, naligwiradi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Atafika pa malo opunthira tirigu a Nakoni, Uza anatambalitsa dzanja lake kuti agwire Bokosi la Mulungu, chifukwa ngʼombe zinkafuna kugwa. Onani mutuwo |