Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 6:4 - Buku Lopatulika

4 Potuluka nalo tsono pamodzi ndi likasa la Mulungu m'nyumba ya Abinadabu ili pachitunda, Ahiyo anatsogolera likasalo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Potuluka nalo tsono pamodzi ndi likasa la Mulungu m'nyumba ya Abinadabu ili pachitunda, Ahiyo anatsogolera likasalo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 imene idaanyamula Bokosi lachipanganolo kuchoka nalo ku nyumba ya Abinadabu ija ku phiri. Ahiyo ankayenda patsogolo pa Bokosi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 imene inanyamula Bokosi la Mulungu, ndipo Ahiyo mwana wa Abinadabu ankayenda patsogolo pake.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 6:4
3 Mawu Ofanana  

Ndipo iwo ananyamulira likasa la Mulungu pa galeta watsopano, atalitulutsa m'nyumba ya Abinadabu, ili pachitunda, ndipo Uza ndi Ahiyo ana a Abinadabu anayendetsa ng'ombe za pa galeta watsopanoyo.


Ndipo anatengera likasa la Mulungu pa galeta watsopano kuchokera kunyumba ya Abinadabu; ndi Uza ndi Ahiyo anayendetsa ng'ombe za pa galetayo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa