2 Samueli 6:18 - Buku Lopatulika18 Pamene Davide adatsiriza kupereka nsembe yopsereza ndi zoyamika, iye anawadalitsa anthuwo m'dzina la Yehova wa makamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pamene Davide adatsiriza kupereka nsembe yopsereza ndi zoyamika, iye anawadalitsa anthuwo m'dzina la Yehova wa makamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Atatsiriza kupereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjanozo, adadalitsa anthu m'dzina la Chauta Wamphamvuzonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Atatsiriza kupereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano, iye anadalitsa anthu mʼdzina la Yehova Wamphamvuzonse. Onani mutuwo |