2 Samueli 5:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Afilisti anakweranso kachiwiri, natanda m'chigwa cha Refaimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Afilisti anakweranso kachiwiri, natanda m'chigwa cha Refaimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Nthaŵi ina Afilisti adabweranso, nandanda m'chigwa chija cha Refaimu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Nthawi inanso Afilisti anabweranso namwazikana mʼChigwa cha Refaimu; Onani mutuwo |