2 Samueli 5:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo iwo anasiya kumeneko mafano ao; Davide ndi anyamata ake nawachotsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo iwo anasiya kumeneko mafano ao; Davide ndi anyamata ake nawachotsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Afilisti adasiya mafano ao kumeneko, ndipo Davide ndi anthu ake adatenga mafanowo napita nawo kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Afilisti anasiya mafano awo kumeneko ndipo Davide ndi ankhondo ake anawatenga. Onani mutuwo |