2 Samueli 5:17 - Buku Lopatulika17 Koma pamene Afilisti anamva kuti adamdzoza Davide mfumu ya Israele, Afilisti onse anakwera kukafuna Davide; ndipo Davide anachimva natsikira kungaka kuja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Koma pamene Afilisti anamva kuti adamdzoza Davide mfumu ya Israele, Afilisti onse anakwera kukafuna Davide; ndipo Davide anachimva natsikira kungaka kuja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Afilisti atamva kuti Davide wadzozedwa kukhala mfumu yolamulira dziko la Aisraele, adapita kukamfunafuna. Koma Davide atamva zimenezo, adatsikira ku linga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Afilisti atamva kuti Davide wadzozedwa kukhala mfumu ya Israeli, iwo anapita mwamphamvu kukamusakasaka. Koma Davide atamva zimenezi anakalowa mu linga. Onani mutuwo |