2 Samueli 5:1 - Buku Lopatulika1 Pomwepo mafuko onse a Israele anabwera kwa Davide ku Hebroni, nalankhula nati, Taonani, ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pomwepo mafuko onse a Israele anabwera kwa Davide ku Hebroni, nalankhula nati, Taonani, ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake mafuko onse a Aisraele adadzasonkhana kwa Davide ku Hebroni. Adamuuza kuti, “Ifetu ndi inuyo tili magazi amodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mafuko onse a Israeli anabwera kwa Davide ku Hebroni ndipo anati, “Ife ndife mafupa ndi mnofu wanu. Onani mutuwo |