2 Samueli 3:30 - Buku Lopatulika30 Motero Yowabu ndi Abisai mbale wake adapha Abinere, popeza iye adapha mbale wao Asahele ku Gibiyoni, kunkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Motero Yowabu ndi Abisai mbale wake adapha Abinere, popeza iye adapha mbale wao Asahele ku Gibiyoni, kunkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Choncho Yowabu ndi mbale wake Abisai adapha Abinere chifukwa choti Abinereyo anali ataŵaphera mbale wao Asahele pa nkhondo ya ku Gibiyoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 (Yowabu ndi mʼbale wake Abisai anapha Abineri chifukwa iye anapha mʼbale wawo Asaheli ku nkhondo ku Gibiyoni). Onani mutuwo |