2 Samueli 3:20 - Buku Lopatulika20 Abinere nafika kwa Davide ku Hebroni, ali ndi anthu makumi awiri. Ndipo Davide anawakonzera Abinere ndi anthu okhala naye madyerero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Abinere nafika kwa Davide ku Hebroni, ali ndi anthu makumi awiri. Ndipo Davide anawakonzera Abinere ndi anthu okhala naye madyerero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Pambuyo pake Abinere adabwera ndi anthu makumi aŵiri kwa Davide ku Hebroni. Davideyo adakonzera madyerero Abinere ndi anthu makumi aŵiri amene anali nawowo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Abineri, amene anali ndi anthu makumi awiri, atafika kwa Davide ku Hebroni, Davide anamukonzera phwando pamodzi ndi anthu ake. Onani mutuwo |