Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 24:23 - Buku Lopatulika

23 zonsezi, mfumu, Arauna akupatsani mfumu. Ndipo Arauna anati kwa mfumu, Yehova Mulungu wanu akulandireni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 zonsezi, mfumu, Arauna akupatsani mfumu. Ndipo Arauna anati kwa mfumu, Yehova Mulungu wanu akulandireni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Zonsezi Arauna adazipereka kwa mfumu, ndipo adapitiriza nati, “Chauta Mulungu wanu, alandire nsembe zanuzo.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Inu mfumu, Arauna akupereka zonsezi kwa inu mfumu.” Arauna anatinso kwa iye, “Yehova Mulungu wanu akuvomerezeni.”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 24:23
10 Mawu Ofanana  

M'malo mwa makolo ako mudzakhala ana ako, udzawaika akhale mafumu m'dziko lonse lapansi.


Koma mfulu aganizira zaufulu, nakhazikika m'zaufulu zomwe.


Zoweta za Kedara zidzasonkhana kwa iwe, nkhosa zamphongo za Nebayoti zidzakutumikira; izo zidzafika ndi kulandiridwa paguwa langa la nsembe; ndipo ndidzakometsa nyumba ya ulemerero wanga.


Kunena za nsembe za zopereka zanga, aphera nsembe yanyama, naidya; koma Yehova sazilandira; tsopano adzakumbukira mphulupulu yao, nadzalanga zochimwa zao; adzabwerera kunka ku Ejipito.


inunso ngati miyala yamoyo mumangidwa nyumba ya uzimu, kuti mukhale ansembe oyera mtima, akupereka nsembe zauzimu, zolandiridwa ndi Mulungu mwa Yesu Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa