2 Samueli 24:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo Davide anakwerako monga mwa kunena kwa Gadi, monga adalamulira Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo Davide anakwerako monga mwa kunena kwa Gadi, monga adalamulira Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Atamva mau a Gadiwo, Davide adapita monga momwe Chauta adaalamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ndipo Davide anapita monga momwe Yehova anamulamulira kudzera mwa Gadi. Onani mutuwo |