2 Samueli 24:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo pouka Davide m'mawa mau a Yehova anafika kwa mneneri Gadi, mlauli wa Davide, kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo pouka Davide m'mawa mau a Yehova anafika kwa mneneri Gadi, mlauli wa Davide, kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono Davide atadzuka m'maŵa, Chauta adalankhula ndi Gadi, mneneri wa Davide, namuuza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Davide asanadzuke mmawa mwake mawu a Yehova anafika kwa mneneri Gadi, mlosi wa Davide kuti, Onani mutuwo |