Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 23:31 - Buku Lopatulika

31 Abiyaliboni Mwarabati, Azimaveti Mbahurimi;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Abiyaliboni Mwarabati, Azimaveti Mbahurimi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Abiyaliboni Mwaraba, Azimaveti wa ku Bahurimu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Abi-Aliboni Mwaribati, Azimaveti Mbarihumi,

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 23:31
6 Mawu Ofanana  

Ndipo pakufika mfumu Davide ku Bahurimu, onani, panatuluka pamenepo munthu wa banja la nyumba ya Saulo, dzina lake ndiye Simei, mwana wa Gera; iyeyu anatulukako, nayenda natukwana.


Ndipo mwamuna wakeyo anapita naye, nanka nalira, namtsata kufikira ku Bahurimu. Pomwepo Abinere ananena naye, Choka, bwerera; ndipo anabwerera.


Mkulu wao ndiye Ahiyezere, ndi Yowasi, ana a Semaa wa ku Gibea; ndi Yeziyele, ndi Peleti, ana a Azimaveti; ndi Beraka, ndi Yehu wa ku Anatoti,


Ndipo woyang'anira chuma cha mfumu ndiye Azimaveti mwana wa Adiyele, ndi woyang'anira wa chuma cha m'minda, m'mizinda ndi m'midzi, ndi nyumba za nsanja, ndiye Yonatani mwana wa Uziya;


ndi Betaraba, ndi Zemaraimu, ndi Betele;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa