2 Samueli 23:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Davide analakalaka nati, Ha! Wina akadandipatsa madzi a m'chitsime cha ku Betelehemu chili pachipatapo! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Davide analakalaka nati, Ha! Wina akadandipatsa madzi a m'chitsime cha ku Betelehemu chili pachipatapo! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Tsono Davide adalankhula molakalaka kuti, “Ha, wina akadandipatsa madzi akumwa a m'chitsime chimene chili ku chipata ku Betelehemu kuti ndimwe!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Davide analakalaka madzi ndipo anati, “Haa, pakanapezeka munthu wokanditungira madzi a mʼchitsime chomwe chili pafupi ndi chipata cha ku Betelehemu!” Onani mutuwo |