2 Samueli 23:14 - Buku Lopatulika14 Pamenepo Davide anali m'linga, ndi boma la Afilisti linali mu Betelehemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Pamenepo Davide anali m'linga, ndi boma la Afilisti linali m'Betelehemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pamenepo nkuti Davide ali m'phanga muja, ndipo kagulu kankhondo ka Afilisti kali ku Betelehemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Nthawi imeneyo Davide anali mu linga, ndipo boma la Afilisti linali ku Betelehemu. Onani mutuwo |