2 Samueli 23:12 - Buku Lopatulika12 Koma iyeyo anaima pakati pamundawo, nautchinjiriza, napha Afilistiwo. Ndipo Yehova anachititsa chipulumutso chachikulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma iyeyo anaima pakati pa mundawo, nautchinjiriza, napha Afilistiwo. Ndipo Yehova anachititsa chipulumutso chachikulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Koma iyeyo adaima pakatimpakati pa mundawo nautchinjiriza, ndipo adapha Afilistiwo, chifukwa Chauta adampambanitsa kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Koma Sama anayima pakati pa mundawo. Iye anawuteteza nakantha Afilistiwo ndipo Yehova anawapambanitsa koposa. Onani mutuwo |