2 Samueli 21:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anati kwa mfumu, Munthu uja anatitha natilingalira pa ife chotionongera kuti tisakhalenso m'malire ali onse a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anati kwa mfumu, Munthu uja anatitha natilingalira pa ife chotionongera kuti tisakhalenso m'malire ali onse a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Iwo adayankha kuti, “Saulo adaafuna kutiwonongeratu, ndipo adaakonza zoti titheretu m'dziko lonse la Israele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iwo anayankha mfumu kuti, “Tsono za munthu amene anatiwononga ndi kukonza chiwembu choti titheretu ndi kukhala wopanda malo mu Israeli, Onani mutuwo |
Ndipo atapita masabata makumi asanu ndi limodzi mphambu awiri wodzozedwayo adzalikhidwa, nadzakhala wopanda kanthu; ndi anthu a kalonga wakudzayo adzaononga mzinda ndi malo opatulika; ndi kutsiriza kwake kudzakhala kwa chigumula, ndi kufikira chimaliziro kudzakhala nkhondo; chipasuko chalembedweratu.