2 Samueli 20:16 - Buku Lopatulika16 Pamenepo mkazi wanzeru wa m'mzindamo anafuula, kuti, Imvani, imvani; munene kwa Yowabu, Bwerani pafupi kuno kuti ndilankhule nanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pamenepo mkazi wanzeru wa m'mudzimo anafuula, kuti, Imvani, imvani; munene kwa Yowabu, Bwerani pafupi kuno kuti ndilankhule nanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndiye mkazi wina wanzeru adayamba kuitana mumzindamo kuti, “Tamverani! Tamverani! Tauzani aYowabu abwere kuno kuti ndilankhule nawo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 mayi wina wanzeru anafuwula kuchokera mu mzindawo, “Tamverani! Tamverani! Muwuzeni Yowabu abwere pano kuti ndiyankhule naye.” Onani mutuwo |