Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 2:25 - Buku Lopatulika

25 Ndipo ana a Benjamini anaunjikana pamodzi kutsata Abinere, nakhala gulu limodzi, naima pamwamba pa chitunda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Ndipo ana a Benjamini anaunjikana pamodzi kutsata Abinere, nakhala gulu limodzi, naima pamwamba pa chitunda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Abenjamini adasonkhana pamodzi kuthandiza Abinere, ndipo adapanga gulu limodzi lankhondo, nakaima pamwamba pa phiri.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Pamenepo anthu a fuko la Benjamini anasonkhana kudzathandiza Abineri. Iwo anapanga gulu ndipo anayima pamwamba pa phiri.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 2:25
2 Mawu Ofanana  

Koma Yowabu ndi Abisai anampirikitsa Abinere; ndipo dzuwa linawalowera pofika ku chitunda cha Ama, chakuno cha Giya, panjira ya ku chipululu cha Gibiyoni.


Pomwepo Abinere anaitana Yowabu nati, Kodi lupanga lidzaononga chionongere? Sudziwa kodi kuti kutha kwake kudzakhala udani ndithu? Tsono udzakhalanso nthawi yanji osauza anthu kubwerera pakutsata abale ao?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa