2 Samueli 19:42 - Buku Lopatulika42 Ndipo anthu onse a Yuda anayankha anthu a Israele. Chifukwa mfumu ili ya chibale chathu; tsono mulikukwiyiranji pa mlandu umenewu? Tinadya konse za mfumu kodi? Kapena kodi anatipatsa mtulo uliwonse? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ndipo anthu onse a Yuda anayankha anthu a Israele. Chifukwa mfumu ili ya chibale chathu; tsono mulikukwiyiranji pa mlandu umenewu? Tinadya konse za mfumu kodi? Kapena kodi anatipatsa mtulo uliwonse? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Ayuda adayankha Aisraelewo kuti, “Chifukwa chake nchakuti mfumuyi ndi mbale wathu weniweni. Inu chakukwiyitsani nchiyani pamenepa? Kodi mfumu taidyera chiyani? Nanga yatipatsa mphatso yanji?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Ayuda onse anayankha Aisraeli kuti, “Ife timachita zimenezi chifukwa mfumu ndi mʼbale wathu. Nʼchifukwa chiyani inu mwapsa mtima ndi zimenezi? Kodi ife tinadya chakudya chilichonse cha mfumu? Kodi chilipo chimene ife tatenga kukhala chathu?” Onani mutuwo |