2 Samueli 19:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo mfumu inafunda nkhope yake, nilira ndi mau okweza, Mwana wanga Abisalomu, Abisalomu, mwana wanga, mwana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo mfumu inafunda nkhope yake, nilira ndi mau okweza, Mwana wanga Abisalomu, Abisalomu, mwana wanga, mwana wanga, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mfumu idaphimba kumaso, nimalira kuti, “Kalanga ine, mwana wanga Abisalomu, iwe Abisalomu mwana wanga, mwana wanga!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mfumu inaphimba nkhope yake ndipo inalira mofuwula, “Iwe mwana wanga Abisalomu! Iwe Abisalomu, mwana wanga, mwana wanga!” Onani mutuwo |