2 Samueli 17:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Husai ananena ndi Abisalomu, Uphungu anaupangira lero Ahitofele suli wabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Husai ananena ndi Abisalomu, Uphungu anaupangira lero Ahitofele suli wabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Husai adauza Abisalomu kuti, “Ulendo uno, malangizo amene wakupatsani Ahitofele si abwino konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Husai anayankha Abisalomu kuti, “Malangizo amene Ahitofele wapereka si abwino pa nthawi ino. Onani mutuwo |