2 Samueli 17:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo mkazi anatenga chivundikiro nachiika pakamwa pa chitsime, napapasapo lipande la tirigu; momwemo sichinadziwike. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo mkazi anatenga chivundikiro nachiika pakamwa pa chitsime, napapasapo lipande la tirigu; momwemo sichinadziwika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tsono mkazi wa munthu uja adatenga chivundikiro, nachiika pamwamba pa chitsimecho, nkuyanikapo tirigu, kotero kuti chitsimecho sichinkadziŵika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mkazi wake anatenga chophimba ndipo anachiyika pamwamba pa chitsimecho nawazapo tirigu. Palibe amene anadziwa chilichonse za izi. Onani mutuwo |