2 Samueli 15:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo Davide ananena naye, Ukapita pamodzi ndi ine udzandilemetsa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo Davide ananena naye, Ukapita pamodzi ndi ine udzandilemetsa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Davide adamuuza kuti, “Ukapita nane, sizindithandiza kwenikweni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Davide anati kwa iye, “Ngati iwe upite ndi ine, udzakhala chondilemetsa. Onani mutuwo |
Lero ndili nazo zaka makumi asanu ndi atatu; kodi ndikhoza kuzindikiranso kusiyanitsa zabwino ndi zoipa? Mnyamata wanu ndikhoza kodi kuzindikira chimene ndidya kapena kumwa? Kodi ndikhozanso kumva mau a amuna ndi akazi oimba? Chifukwa ninji tsono mnyamata wanu ndidzakhalanso wolemetsa mbuye wanga mfumu.