2 Samueli 15:26 - Buku Lopatulika26 Koma Iye akatero kuti, Sindikondwera nawe konse; onani, ndine pano, andichitire chimene chimkomera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Koma Iye akatero kuti, Sindikondwera nawe konse; onani, ndine pano, andichitire chimene chimkomera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Koma akapanda kukondwera nane, chabwino, andichite zomwe zimkomere.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Koma iye anati, ‘Akapanda kukondwera nane,’ chabwino, andichite chimene chimukomere.” Onani mutuwo |