2 Samueli 15:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo mthenga unafika kwa Davide nuti, Mitima ya anthu a Israele itsata Abisalomu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo mthenga unafika kwa Davide nuti, Mitima ya anthu a Israele itsata Abisalomu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsiku lina wamthenga adafika kwa Davide kudzanena kuti, “Aisraele onse ali pambuyo pa Abisalomu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Munthu wina anabweretsa uthenga ndi kudzamuwuza Davide kuti, “Mitima ya Aisraeli onse ili pa Abisalomu.” Onani mutuwo |