2 Samueli 14:31 - Buku Lopatulika31 Pamenepo Yowabu ananyamuka nafika kwa Abisalomu kunyumba yake, nanena naye, Chifukwa ninji anyamata anu anatentha za m'munda mwanga; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Pamenepo Yowabu ananyamuka nafika kwa Abisalomu kunyumba yake, nanena naye, Chifukwa ninji anyamata anu anatentha za m'munda mwanga; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Tsono Yowabu adanyamuka kupita kunyumba kwa Abisalomu, nakamufunsa kuti, “Bwanji atumiki ako atentha munda wanga?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Ndipo Yowabu anapita ku nyumba ya Abisalomu ndipo anati kwa iye, “Nʼchifukwa chiyani antchito ako atentha munda wanga?” Onani mutuwo |