Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 13:35 - Buku Lopatulika

35 Ndipo Yonadabu ananena ndi mfumu, Onani, ana aamuna a mfumu afika; monga ananena mnyamata wanu, momwemo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

35 Ndipo Yonadabu ananena ndi mfumu, Onani, ana amuna a mfumu afika; monga ananena mnyamata wanu, momwemo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

35 Atamva zimenezi Yonadabu adauza mfumu kuti, “Ana a mfumu abwera. Amfumu, monga momwe ndinakuuzirani muja, ndi m'mene zayendera.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

35 Yehonadabu anati kwa mfumu, “Taonani ana a mfumu afika. Zachitika monga momwe mtumiki wanu ananenera.”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 13:35
2 Mawu Ofanana  

Koma Abisalomu anathawa. Ndipo mnyamata wakudikira anatukula maso ake nayang'ana, ndipo onani, m'mbuyo mwake anthu ambiri analikubwera m'njira yolambalala phiri.


Ndipo kunali pakutsiriza iye kulankhula, onani, pomwepo ana aamuna a mfumu anafika, nakweza mau ao, nalira misozi; ndi mfumu yomwe ndi anyamata ake analira ndi kulira kwakukulu ndithu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa