2 Samueli 13:33 - Buku Lopatulika33 Chifukwa chake tsono mfumu mbuye wanga asasauke mtima ndi chinthuchi, ndi kuganiza kuti ana aamuna onse a mfumu afa; pakuti Aminoni yekha wafa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Chifukwa chake tsono mfumu mbuye wanga asasauke mtima ndi chinthuchi, ndi kuganiza kuti ana amuna onse a mfumu afa; pakuti Aminoni yekha wafa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Nchifukwa chake tsono mbuyanga mfumu, musavutike ndi maganizo oti ana anu onse aamuna aphedwa. Aminoni yekha ndiye waphedwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Mbuye wanga mfumu musavutike ndi maganizo ndi nkhani yoti ana onse a mfumu afa. Wafa ndi Amnoni yekha.” Onani mutuwo |