2 Samueli 13:31 - Buku Lopatulika31 Pamenepo mfumu inanyamuka ning'amba zovala zake nigona pansi, ndipo anyamata ake onse anaimirirapo ndi zovala zao zong'ambika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Pamenepo mfumu inanyamuka ning'amba zovala zake nigona pansi, ndipo anyamata ake onse anaimirirapo ndi zovala zao zong'ambika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Pompo mfumu idadzuka, ning'amba zovala zake, nkudzigwetsa pansi. Atumiki ake onse amene anali pafupi naye, nawonso adang'amba zovala zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Mfumu inayimirira, ningʼamba zovala zake ndi kugona pa dothi. Antchito ake onse anayimirira pomwepo atangʼamba zovala zawo. Onani mutuwo |