2 Samueli 12:8 - Buku Lopatulika8 ndinakupatsa nyumba ya mbuye wako, ndi akazi a mbuye wako pa chifukato chako, ndinakupatsanso nyumba ya Israele ndi ya Yuda; ndipo zimenezi zikadakuchepera ndikadakuonjezera zina zakutizakuti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 ndinakupatsa nyumba ya mbuye wako, ndi akazi a mbuye wako pa chifukato chako, ndinakupatsanso nyumba ya Israele ndi ya Yuda; ndipo zimenezi zikadakuchepera ndikadakuonjezera zina zakutizakuti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndidakupatsa banja la mbuyako, kudzanso akazi a mbuyako kuti akhale m'manja mwako, ndipo ndidakupatsanso mtundu wa Israele pamodzi ndi fuko la Yuda. Tsono zimenezi zikadakuchepera, ndikadakuwonjezera zina zambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndinakupatsanso banja la mbuye wako ndiponso akazi a mbuye wako mʼmanja mwako. Ine ndinakupatsanso banja la Israeli ndi Yuda. Ndipo ngati zinthu zonse izi zinali zochepa, Ine ndikanakupatsa zambiri. Onani mutuwo |