2 Samueli 12:6 - Buku Lopatulika6 ndipo adzabwezera mwa mwanawankhosayo ena anai, chifukwa anachita ichi osakhala nacho chifundo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 ndipo adzabwezera mwa mwanawankhosayo ena anai, chifukwa anachita ichi osakhala nacho chifundo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ndipo pa mwanawankhosayo abwezere ena anai, chifukwa chochita zotere, ndiponso popeza kuti analibe chifundo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iye ayenera kulipira mwana wankhosa wamkaziyo kanayi, chifukwa anachita chinthu chimenechi ndipo analibe chifundo.” Onani mutuwo |