2 Samueli 12:12 - Buku Lopatulika12 Pakuti iwe unachichita m'tseri; koma Ine ndidzachita chinthu ichi pamaso pa Aisraele onse, dzuwa lili nde. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti iwe unachichita m'tseri; koma Ine ndidzachita chinthu ichi pamaso pa Aisraele onse, dzuwa lili nde. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Iwe unkachita zimenezo m'seri, koma Ine ndidzazichita pamaso pa Aisraele onse, masana ndithu.’ ” Apo Davide adauza Natani kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iwe unachita zimenezi mwamseri koma Ine ndidzachita izi masanasana Aisraeli onse akuona.’ ” Onani mutuwo |