2 Samueli 12:10 - Buku Lopatulika10 Chifukwa chake tsono lupanga silidzachoka pa nyumba yako nthawi zonse, popeza unandipeputsa Ine, nudzitengera mkazi wa Uriya Muhiti akhale mkazi wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chifukwa chake tsono lupanga silidzachoka pa nyumba yako nthawi zonse, popeza unandipeputsa Ine, nudzitengera mkazi wa Uriya Muhiti akhale mkazi wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Nchifukwa chake tsono nkhondo siidzachoka pabanja pako chifukwa wandinyoza Ine, ndipo wakwatira mkazi wa Uriya Muhiti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo tsopano lupanga silidzachoka pa nyumba yako, chifukwa unandinyoza ine ndi kutenga mkazi wa Uriya Mhiti kukhala wako.’ Onani mutuwo |