2 Samueli 11:9 - Buku Lopatulika9 Koma Uriya anagona pa khomo la nyumba ya mfumu pamodzi ndi anyamata onse a mbuye wake, osatsikira kunyumba yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma Uriya anagona pa khomo la nyumba ya mfumu pamodzi ndi anyamata onse a mbuye wake, osatsikira kunyumba yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma Uriya adagona pakhomo pa nyumba ya mfumu pamodzi ndi antchito onse a mbuye wake, sadapite kunyumba kwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma Uriya anagona pa chipata cha nyumba yaufumu pamodzi ndi antchito onse a mbuye wake ndipo sanapite ku nyumba yake. Onani mutuwo |