Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




2 Samueli 11:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Koma Uriya anagona pa chipata cha nyumba yaufumu pamodzi ndi antchito onse a mbuye wake ndipo sanapite ku nyumba yake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Koma Uriya anagona pa khomo la nyumba ya mfumu pamodzi ndi anyamata onse a mbuye wake, osatsikira kunyumba yake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Koma Uriya anagona pa khomo la nyumba ya mfumu pamodzi ndi anyamata onse a mbuye wake, osatsikira kunyumba yake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Koma Uriya adagona pakhomo pa nyumba ya mfumu pamodzi ndi antchito onse a mbuye wake, sadapite kunyumba kwake.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 11:9
6 Mawu Ofanana  

Davide atawuzidwa kuti, “Uriya sanapite ku nyumba yake.” Iye anafunsa kuti, “Kodi iwe sunachokera kutali? Nʼchifukwa chiyani sunapite ku nyumba yako?”


Davide anayitana Uriya nadya ndi kumwa naye, ndipo Davide anamuledzeretsa. Koma madzulo Uriya anapita kukagona pa mphasa pamodzi ndi antchito a mbuye wake. Iye sanapite ku nyumba yake.


Ndipo Mfumu Rehobowamu anapanga zishango zamkuwa mʼmalo mwake, nazipereka mʼmanja mwa olamulira alonda a pa khomo pa nyumba ya mfumu.


Nthawi zonse mfumu ikamapita ku Nyumba ya Yehova, alonda ankanyamula zishangozo, kenaka ankazisunga mʼchipinda cha alonda.


Palibe nzeru, palibe kumvetsa bwino, palibenso uphungu, zimene zingapambane Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa