2 Samueli 11:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo mthengawo unati kwa Davide, Anthuwo anatipambana natulukira kwa ife kumundako, koma tinawagwera kufikira polowera kuchipata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo mthengawo unati kwa Davide, Anthuwo anatilaka natulukira kwa ife kumundako, koma tinawagwera kufikira polowera kuchipata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Adauza Davide kuti, “Adani athu adaatipambana, ndipo adaatuluka kukalimbana nafe ku thengo. Koma ife tidaŵabweza mpaka ku khomo lakuchipata. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Mthengayo anati kwa Davide, “Anthuwo anatiposa mphamvu ndipo anabwera kudzalimbana nafe poyera, koma ife tinawabwezera ku chipata cha mzindawo. Onani mutuwo |