Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 1:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo iye pakucheukira m'mbuyo mwake anandiona, nandiitana. Ndipo ndinayankha, Ndine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo iye pakucheukira m'mbuyo mwake anandiona, nandiitana. Ndipo ndinayankha, Ndine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Tsono Saulo atacheuka nandiwona, adandiitana. Ndidavomera kuti, ‘Ŵaŵa.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Pamene anatembenuka ndi kundiona ine, iye anandiyitana, ndipo ndinati, ‘Kodi ndichite chiyani?’ ”

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 1:7
7 Mawu Ofanana  

Mnyamata wakumuuzayo nati, Pamene ndinangoyenda paphiri la Gilibowa, ndinaona, Saulo alikuyedzamira nthungo yake, ndi magaleta ndi apakavalo anamyandikiza.


Nanena, Ndiwe yani? Ndipo ndinayankha kuti, Ndine Mwamaleke.


Ndipo Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Saulo, anafika kwa Davide, nagwa nkhope yake pansi, namlambira. Ndipo Davide anati, Mefiboseti! Nayankha iye, Ndine mnyamata wanu.


Ndipo ndinamva mau a Ambuye akuti, Ndidzatumiza yani, ndipo ndani adzatimukira ife? Ndipo ine ndinati, Ndine pano; munditumize ine.


Iwo amene sanafunse za Ine andifunafuna; ndi iwo amene sanandipwaire andipeza; ndinati, Taonani Ine, taonani Ine, kwa mtundu umene sunatchule dzina langa.


Pamenepo anaitana msanga mnyamata wake wosenza zida zake, nanena naye, Solola lupanga lako nundiphe, angamanenere anthu, ndi kuti, Anamupha ndi mkazi. Nampyoza mnyamata wake, nafa iye.


Ndipo Saulo anati, Imva tsopano iwe mwana wa Ahitubi. Nayankha iye, Ndine, mbuye wanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa