2 Akorinto 9:1 - Buku Lopatulika1 Pakutitu za utumiki wa kwa oyera mtima sikufunika kwa ine kulembera inu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pakutitu za utumiki wa kwa oyera mtima sikufunika kwa ine kulembera inu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Nkosafunikira kuti ndikulembereni za zopereka zothandizira anthu a Mulungu a ku Yudeya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Nʼkosafunika kuti ndikulembereni za utumiki othandiza anthu a Mulungu. Onani mutuwo |