2 Akorinto 8:15 - Buku Lopatulika15 Kuti pakhale chilingano; monga kwalembedwa, Wosonkhetsa chambiri sichinamtsalire; ndi iye wosonkhetsa pang'ono sichinamsowe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Kuti pakhale chilingano; monga kwalembedwa, Wosonkhetsa chambiri sichinamtsalira; ndi iye wosonkhetsa pang'ono sichinamsowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Paja Malembo akuti, “Amene adapata zambiri, sizidamchulukire, amene adapata pang'ono, sizidamchepere.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 monga kwalembedwa kuti, “Iye amene anatola zambiri sizinamutsalireko ndipo amene anatola pangʼono sizinamuchepere.” Onani mutuwo |